NSINJIRO ZA CHIYANKHULO
Kodi nsinjiro za chiyankhulo ndi chiyani?
M'mawu a m'Chichewa amene amasangalatsa powamva pamene tikulemba
kapena kuyankhula amatchedwa nsinjiro za chiyankhulo popeza amakometsa
chiyankhulo monganso m'mene nsinjiro zimatha kukometsera ndiwo.
ZITSANZO ZA NSINJIRO ZA CHIYANKHULO
- zining'a,
-
ntchedzero (zifanifani),
- miseketso,
- mizimbayitso,
- voko
- nkhambakamwa.